Job 11:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
achikhala adaakuululira zinsinsi za nzeru! Paja Iye uja nzeru zake ndi zozama zedi. Udziŵe tsono kuti Mulungu akukulanga pang'ono, mosalingana nkuchuluka kwa zolakwa zako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nakufotokozere zinsinsi za nzeru, popeza zipindikapindika machitidwe ao! Chifukwa chake dziwa kuti Mulungu akuiwalira mphulupulu zina.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndi kukuwululira chinsinsi cha nzeru yake, pakuti nzeru yeniyeni ili ndi mbali ziwiri. Dziwa izi: Mulungu wayiwala machimo ako ena.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nakufotokozere zinsinsi za nzeru, Popeza zipindika-pindika macitidwe ao! Cifukwa cace dziwa kuti Mulungu akuiwalira mphulupulu zina.