Job 11:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Malire a nzeru zake ali kutali kuposa mlengalenga. Nanga iwe ungachitepo chiyani? Malire a nzeru zake ndi ozama kupitirira dziko la anthu akufa. Nanga iwe ungathe kudziŵapo chiyani?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kumpeza kutalika ngati kumwamba, ungachitenji? Kuzama ngati kumanda, ungadziwenji?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zili kutali kupambana mayiko akumwamba, nanga ungachite chiyani? Ndi zakuya kupambana kuya kwa manda, nanga ungadziwe chiyani?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kumpeza kutalika ngati kumwamba, ungacitenji? Kuzama ngati kumanda, ungadziwenji?