Job 11:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muyeso wa nzeru zake ndi wautali kupambana kutalika kwa dziko lapansi, ndi kupingasa kwa nyanja zamchere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muyeso wake utalikira utali wake wa dziko lapansi, chitando chake chiposa cha nyanja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Muyeso wa nzeru zake ndi wautali kupambana dziko lapansi ndipo ndi wopingasa kupambana nyanja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muyeso wace utalikira utali wace wa dziko lapansi, Citando cace ciposa ca nyanja.