Job 12:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi suja khutu ndiye limamva mau, monga m'mene lilime ndiye limalaŵa chakudya?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'khutumu simuyesa mau, monga m'kamwa mulawa chakudya chake?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi khutu sindiye limene limamva mawu monga mmene lilime limalawira chakudya?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'khutumu simuyesa mau, Monga m'kamwa mulawa cakudya cace?