Job 12:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Koma Mulungu ali ndi nzeru ndi mphamvu zopambana. Ali ndi uphungu wabwino, ndi kumvetsa zinthu zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwa Iye kuli nzeru ndi mphamvu; uphungu ndi luntha ali nazo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kwa Mulungu ndiye kuli nzeru ndi mphamvu; uphungu ndi kumvetsa zinthu ndi zake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kwa Iye kuli nzeru ndi mphamvu; Uphungu ndi luntha ali nazo.