Job 12:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amamasula am'ndende a mafumu, ndipo amaŵamanga mafumuwo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amasula chomangira cha mafumu, nawamangira nsinga m'chuuno mwao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amachotsa zingwe zimene mafumu anawamanga nazo ndipo amawamanga lamba mʼchiwuno mwawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amasula comangira ca mafumu, Nawamangira nsinga m'cuuno mwao.