Job 12:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amakuza mitundu ina ya anthu, koma inanso amaiwononga. Amachulukitsa mafuko, nkuŵamwazanso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
achulukitsa amitundu, nawaononganso; abalalikitsa amitundu, nawabwezanso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amakuza mitundu ya anthu ndipo amayiwononganso; amachulukitsa mitundu ya anthu ndipo amayimwazanso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Acurukitsa amitundu, nawaononganso; Abalalikitsa amitundu, nawabwezanso.