Job 12:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amasandutsa atsogoleri kuti akhale zitsiru, ndi kumaŵayendetsa m'thengo mopanda njira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Awachotsera akulu a anthu a padziko mtima wao, nawasokeretsa m'chipululu chopanda njira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amalanda nzeru za atsogoleri a dziko lapansi; amawayendetsa mʼthengo mopanda njira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Awacotsera akulu a anthu a padziko mtima wao, Nawasokeretsa m'cipululu copanda njira.