Job 12:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma inenso ndili nazo nzeru ngati inu nomwe. Inu simundipambana, ai. Aliyense amadziŵa zonse mwanenazi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma inenso ndili nayo nzeru monga inu. Sindingakuchepereni; ndani sadziwa zonga izi?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma inenso ndili nazo nzeru ngati inu; ineyo sindine munthu wamba kwa inu. Ndani amene sadziwa zonse zimene mwanenazi?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma inenso ndiri nayo nzeru monga inu. Sindingakucepereni; Ndani sadziwa zonga izi?