Job 12:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu amene ali pabwino amanyoza mnzake amene ali pa tsoka. Tsokalo limagwa pa amene wayamba kale kugwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthu wosatekeseka apeputsa tsoka mumtima mwake, limlindira woterereka mapazi ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu amene ali pabwino amanyoza anzawo amene ali pa tsoka. Tsokalo limagwa pa amene wayamba kale kugwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthu wosatekeseka apeputsa tsoka mumtima mwace, Limlindira woterereka mapazi ace.