Job 12:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Achifwamba ndiwo amakhala pa mtendere, amene amaputa Mulungu ndiwo amakhala pabwino. Anthuwo amadalira nyonga zao ngati ndiye Mulungu wao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mahema a achifwamba akhala mumtendere, ndi iwo oputa Mulungu alimbika mtima; amene Mulungu amadzazira dzanja lao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nyumba za anthu achifwamba zimakhala pa mtendere, ndipo anthu amene amaputa Mulungu amakhala pabwino, amene amanyamula milungu yawo mʼmanja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mahema a acifwamba akhala mumtendere, Ndi iwo oputa Mulungu alimbika mtima: Amene Mulungu amadzazira dzanja lao.