Job 12:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Koma ufunse kwa nyama zakuthengo, zidzakuphunzitsa. Ufunse mbalame zamumlengalenga, zidzakuuza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tafunsira tsono kwa nyamazo, zidzakulangiza, ndi mbalame za m'mlengalenga, zidzakuuza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma funsa nyama zakuthengo ndipo zidzakuphunzitsa, kapena mbalame zamumlengalenga ndipo zidzakuwuza;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tafunsira tsono kwa nyamazo, zidzakulangiza, Ndi mbalame za m'mlengalenga, zidzakuuza;