Job 12:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Upemphe nzeru kwa zolengedwa za dziko lapansi, zidzakuphunzitsa, ngakhale nsomba zam'nyanja zidzakufotokozera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kapena ulankhule ndi dziko lapansi, lidzakulangiza; ndi nsomba za kunyanja, zidzakufotokozera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kapena uyankhule ndi dziko lapansi ndipo lidzakuphunzitsa, kapena ulole nsomba zamʼnyanja kuti zikufotokozere.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kapena ulankhule ndi dziko lapansi, lidzakulangiza; Ndi nsomba za kunyanja, zidzakufotokozera,