Job 13:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Zonse mukunenazi ndidaziwona ndi maso, ndidazimva ndi makutu anga, ndipo ndidazimvetsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, diso langa lachiona chonsechi; m'khutu mwanga ndachimva ndi kuchizindikira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ndaziona ndi maso anga zonsezi, ndazimva ndi makutu anga ndipo ndazimvetsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani; diso langa laciona conseci; M'khutu mwanga ndacimva ndi kucizindikira.