Job 13:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Miyambi yanuyi ndi yopandapake ngati phulusa. Zimene mukulankhula kuti mudzitchinjirize nazo zili ngati dothi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zikumbutso zanu ndizo miyambi ya mapulusa; zodzikanira zanu zikunga malinga adothi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mawu anu anzeru ali ngati miyambi yopanda tanthauzo; mawu anu odzitchinjirizira ali ngati mpanda wadothi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zikumbutso zanu ndizo miyambi ya mapulusa; Zodzikanira zanu zikunga malinga adothi.