Job 13:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndili wokonzeka kuika moyo wanga pa chiswe, kaya nkufa, ndife basi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndilumirenji mnofu wanga pamano panga, ndi kupereka moyo wanga m'dzanja langa?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa chiyani ndikuyika moyo wanga pa chiswe ndi kutengera mʼmanja moyo wangawu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndilumirenji mnofu wanga pamano panga, Ndi kupereka moyo wanga m'dzanja langa?