Job 13:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi pali yani amene angatsutsane nane? Ngati zili choncho, ndidakangokhala chete, nkufa basi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndaniyo adzatsutsana nane? Ndikakhala chete, ndidzapereka mzimu wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi alipo wina amene angatsutsane nane? ngati zili choncho, ndidzakhala chete ndi kufa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndaniyo adzatsutsana nane? Ndikakhala cete, ndidzapereka mzimu wanga.