Job 13:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muleke kundilanga, kuwopa Inu kusandidetse nkhaŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mundichotsere dzanja lanu kutali, ndi kuopsa kwanu kusandichititse mantha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Muchotse dzanja lanu pa ine, ndipo muleke kundichititsa mantha ndi kuopsa kwanuko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mundicotsere dzanja lanu kutali, Ndi kuopsa kwanu kusandicititse mantha.