Job 13:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa chiyani mukundifulatira? Bwanji mukundiyesa mdani wanu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mubisiranji nkhope yanu, ndi kundiyesa mdani wanu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa chiyani mukundifulatira ndi kundiyesa ine mdani wanu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mubisiranji nkhope yanu, Ndi kundiyesa mdani wanu?