Job 13:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mukundizenga zinthu zondiŵaŵa, umafukula ngakhale zolakwa za pa ubwana wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mundilembera zinthu zowawa, ndi kundipatsa ngati cholowa mphulupulu za ubwana wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Inu mwalemba zinthu zowawa zonditsutsa nazo ndipo mukundipaka machimo a pa ubwana wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mundilembera zinthu zowawa, Ndi kundipatsa ngati colowa mphulupulu za ubwana wanga.