Job 13:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inuyo ndinu okometsa zinthu ndi mabodza. Nonsenu muli ngati asing'anga apakamwa chabe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma inu ndinu opanga zabodza, asing'anga opanda pake inu nonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma inu mukundipaka mabodza; nonsenu ndinu asingʼanga opanda phindu!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma inu ndinu opanga zabodza, Asing'anga opanda pace inu nonse.