Job 14:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
momwemonso munthu amagona pansi osadzukanso. Mpaka zamumlengalenga zidzatha, iyeyo sadzadzuka. Palibe aliyense angamdzutse kutulo kwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
momwemo munthu agona pansi, osaukanso; kufikira miyamba kulibe, sadzaukanso, kapena kuutsidwa pa tulo take.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
momwemonso munthu amagona ndipo sadzukanso; mpaka zamlengalenga zidzathe, anthu sadzauka kapena kudzutsidwa ku tulo tawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Momwemo munthu agona pansi, osaukanso; Kufikira miyamba kulibe, sadzaukanso, Kapena kuutsidwa pa tulo tace.