Job 14:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Komabe monga phiri limagwa nkuswekasweka, ndipo thanthwe limasendezeka kuchoka pamalo pake,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo zoonadi, likagwa phiri, latha; ndi thanthwe lisunthika m'malo mwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma monga phiri limakokolokera ndi kuswekasweka ndipo monga thanthwe limasunthira kuchoka pa malo ake,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo zoonadi, likagwa phiri, latha; Ndi thanthwe lisunthika m'malo mwace;