Job 14:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amaphuka ngati duŵa, kenaka nkufota. Sakhalitsa, amathaŵa ngati mthunzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atuluka ngati duwa, nafota; athawa ngati mthunzi, osakhalitsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amaphuka ngati duwa ndipo kenaka amafota; amathawa ngati mthunzi ndipo sakhalitsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Aturuka ngati duwa, nafota; Athawa ngati mthunzi, osakhalitsa.