Job 14:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mumleke tsono kuti apumule, akondweko, akondwerere moyo wake monga amachitira waganyu poweruka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
mumleke osamthira maso, kuti apumule, kuti akondwere nalo tsiku lake monga wolembedwa ntchito.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Inu mumufulatire ndipo mumuleke apumule kufikira atakondwera nawo moyo ngati munthu waganyu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mumleke osamthira maso, kuti apumule, Kuti akondwere nalo tsiku lace monga wolembedwa nchito.