Job 14:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mtengo chiyembekezo chake nchakuti akaudula udzaphukanso, nthambi zake sizidzaleka kuphuka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti akaulikha mtengo pali chiyembekezo kuti udzaphukanso, ndi kuti nthambi yake yanthete siidzasowa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mtengo uli nacho chiyembekezo: ngati wadulidwa, udzaphukiranso ndipo nthambi zake sizidzaleka kuphukira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti akaulikha mtengo pali ciyembekezo kuti udzaphukanso, Ndi kuti nthambi yace yanthete siidzasowa.