Job 16:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu amandinyoza polankhula, amandimenya pa tsaya mwachipongwe, akundichitira upo kuti alimbane nane.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo anandiyasamira pakamwa pao; anandiomba pama ndi kunditonza; asonkhana pamodzi kunditsutsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu amatsekula pakamwa pawo kundikuwiza; amandimenya pa tsaya mwachipongwe ndipo amagwirizana polimbana nane.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo anandiyasamira pakamwa pao; Anandiomba pama ndi kunditonza; Asonkhana pamodzi kunditsutsa.