Job 16:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mivi yake ikundilasa pa mbali zonse. Walasa impso zanga mopanda chifundo, watayira pansi ndulu yanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Eni mauta ake andizinga, ang'amba impso zanga, osazileka; natsanulira pansi ndulu yanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
anthu ake oponya mauta andizungulira. Mopanda kundimvera chisoni, Iye akulasa impsyo zanga ndipo akutayira pansi ndulu yanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Eni mauta ace andizinga, Ang'amba imso zanga, osazileka; Natsanulira pansi ndulu yanga.