Job 16:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Iwe, dziko lapansi, usabise zoipa zimene andichita. Kulira kwanga kofuna thandizo kusalekeke.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Dziko iwe, usakwirire mwazi wanga, ndi kulira kwanga kusowe popumira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Iwe dziko lapansi, usakwirire magazi anga; kulira kwanga kofuna thandizo kusalekeke!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Dziko iwe, usakwirire mwazi wanga, Ndi kulira kwanga kusowe popumira.