Job 16:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikadakulimbitsani ndi mau anga, ndikadakuthuzitsani mtima ndi kuchepetsa zoŵaŵa zanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ndikadakulimbikitsani ndi m'kamwa mwanga, ndi chitonthozo cha milomo yanga chikadatsitsa chisoni chanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo mawu a pakamwa panga akanakulimbikitsani; chitonthozo chochokera pa milomo yanga chikanachepetsa ululu wanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ndikadakulimbikitsani ndi m'kamwa mwanga, Ndi citonthozo ca milomo yanga cikadatsitsa cisoni canu.