Job 16:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ine ndikati ndilankhule, zoŵaŵa zanga sizichepa. Ndikati ndikhale chete, zoŵaŵazo zikhala zilipobe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chinkana ndinena chisoni changa sichitsika; ndipo ndikaleka, chindichokera nchiyani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma ine ndikati ndiyankhule ululu wanga sukuchepa; ndipo ndikati ndikhale chete, ululu wanga sukuchokabe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cinkana ndinena cisoni canga sicitsika; Ndipo ndikaleka, cindicokera nciani?