Job 16:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wandigwira, ndipo wasanduka mdani wanga, umboni woti ndine wolakwa. Ndatsala mafupa okhaokha, ndipo chimenechi chikunditsimikiza kuti ndine wolakwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kundigwira kwanu, ndiko umboni wonditsutsa, kuonda kwanga kundiukira, kuchita umboni pamaso panga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mwandimanga ndipo kundimangako kwakhala umboni; kuwonda kwanga kwandiwukira ndipo kukuchita umboni wonditsutsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kundigwira kwanu, ndiko umboni wonditsutsa, Kuonda kwanga kundiukira, kucita umboni pamaso panga.