Job 16:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu wanding'amba ali chikwiyire, ndipo akudana nane, wachita kulumira mano. Mdani wanga akundituzulira maso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye ananding'amba m'kundida kwake, nakwiya nane, anandikukutira mano; mdani wanga ananditong'olera maso ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu amabwera kwa ine mwankhanza ndipo amadana nane, amachita kulumira mano; mdani wanga amandituzulira maso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iye ananding'amba m'kundida kwace, nakwiya nane, Anandikukutira mano; Mdani wanga ananditong'olera maso ace.