Job 17:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtima wanga wasweka ndipo masiku anga atha, manda andiyasamira kukamwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mzimu wanga watha, masiku anga afafanizika, kumanda kwandikonzekeratu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mtima wanga wasweka, masiku anga atha, manda akundidikira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mzimu wanga watha, masiku anga afafanizika, Kumanda kwandikonzekeratu.