Job 17:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma abwenzi anga amanena kuti usiku ndi usana womwe. Amati, ‘kuŵala ndiye kuli pafupi,’ chonsecho mdima uli goo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zisanduliza usiku ukhale usana; kuunika kuyandikana ndi mdima.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu awa amasandutsa usiku kukhala usana, nthawi ya usiku iwo amati ‘kwatsala pangʼono kucha.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zisanduliza usiku ukhale usana; Kuunika kuyandikana ndi mdima.