Job 17:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzauza dzenje la manda kuti, ‘Iwe ndiwe bambo wanga.’ Ndidzalankhulanso ndi mphutsi kuti, ‘Ndiwe mai wanga,’ kapena kuti, ‘Ndiwe mlongo wanga.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndikati kwa dzenje, Ndiwe atate wanga; kwa mphutsi, Ndiwe mai wanga ndi mlongo wanga;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ngati ndinena kwa dzenje la manda ‘ndinu abambo anga,’ ndiponso kwa mphutsi kuti, ‘ndinu amayi anga’ kapena ‘mlongo wanga,’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikati kwa dzenje, Ndiwe atate wanga; Kwa mphutsi, Ndiwe mai wanga ndi mlongo wanga;