Job 17:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mwatseka mitima yao kuti asamvetsetse bwino zanzeru, choncho musalole kuti iwowo apambane.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mwabisira mtima wao nzeru; chifukwa chake simudzawakuza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mwatseka maganizo awo kuti asamvetse zinthu; choncho simudzawalola kuti apambane.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mwabisira mtima wao nzeru; Cifukwa cace simudzawakuza.