Job 17:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja akuti munthu akapereka abwenzi ake chifukwa cha chuma, ana ake amazunzika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye wakupereka mabwenzi ake ku ukapolo, m'maso mwa ana ake mudzada.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati munthu apereka mnzake chifukwa cha chuma, ana ake sadzaona mwayi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iye wakupereka mabwenzi ace kuukapolo, M'maso mwa ana ace mudzada.