Job 17:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu olungama akudabwa nazo kwambiri zimenezi. Anthu osachimwa akupsera mtima anthu osamvera Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anthu oongoka mtima adzadabwa nacho, ndi munthu wosalakwa adzadziutsa kumtsutsa wonyoza Mulunguyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu olungama akudabwa nazo zimenezi; anthu osachimwa akupsera mtima anthu osapembedza Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anthu oongoka mtima adzadabwa naco, Ndi munthu wosalakwa adzadziutsa kumtsotsa wonyoza Mulunguyo.