Job 17:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe anthu olungama enieni amapitirira m'njira zao, anthu osalakwa amalimbikira kukhalabe oyera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma wolungama asungitsa njira yake, ndi iye wa manja oyera adzakulabe mumphamvu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe anthu olungama adzasunga njira zawo, ndipo anthu a makhalidwe abwino mphamvu zawo zidzanka zikuchuluka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma wolungama asungitsa njira yace, Ndi iye wa manja oyera adzakulabe mumphamvu.