Job 18:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amtchera msampha pansi mobisika, amtchera diŵa m'njira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Msampha woponda umbisikira pansi, ndi msampha wa chipeto panjira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amutchera msampha pansi mobisika; atchera diwa pa njira yake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Msampha woponda umbisikira pansi, Ndi msampha wa cipeto panjira.