Job 18:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaali ndi mphamvu, koma tsopano ali ndi njala. Tsoka likumdikira nthaŵi zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Njala idzatha mphamvu yake, ndi tsoka lidzamkonzekeratu pambali pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mphamvu zake zatha chifukwa cha njala, tsoka likumudikira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Njala idzatha mphamvu yace, Ndi tsoka lidzamkonzekeratu pambali pace.