Job 18:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amuchotsa m'nyumba mwake m'mene ankadalira. Amkokera kwa Imfa, mfumu ya zoopsa zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzazulidwa kuhema kwake kumene anakhulupirira; nadzatengedwa kunka naye kwa mfumu ya zoopsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wachotsedwa mʼnyumba imene ankadalira, ndipo amukokera ku imfa, mfumu ya zoopsa zonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzazulidwa kuhema kwace kumene anakhulupirira; Nadzatengedwa kumka naye kwa mfumu ya zoopsa.