Job 18:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sadzamkumbukiranso kwao kapena kwina kulikonse, dzina lake lidzaiŵalika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chikumbukiro chake chidzatayika m'dziko, ndipo adzasowa dzina kukhwalala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sadzakumbukiridwanso pa dziko lapansi; sadzakhalanso ndi chinthu chomutchukitsa mʼdziko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cikumbukilo cace cidzatayika m'dziko, Ndipo adzasowa dzina kukhwalala.