Job 18:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sadzaona zidzukulu m'banja mwake. Sikudzaoneka ana otsala kumene ankakhalako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sadzakhala naye mwana kapena chidzukulu mwa anthu a mtundu wake, kapena wina wotsalira kumene anakhalako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye alibe ana kapena zidzukulu pakati pa anthu ake, kulibe wotsala kumene iye ankakhala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sadzakhala naye mwana kapena cidzukulu mwa anthu amtundu wace, Kapena wina wotsalira kumene anakhalako.