Job 18:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu akuzambwe adabwa nalo tsoka lakelo, anthu akuvuma nawonso akungopukusa mitu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akudza m'mbuyo adzadabwa nalo tsiku lake, monga aja omtsogolera anagwidwa mantha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu akumadzulo adabwa kwambiri ndi tsoka lake; anthu akummawa agwidwa ndi mantha aakulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akudza m'mbuyo adzadabwa nalo tsiku lace, Monga aja omtsogolera anagwidwa mantha.