Job 18:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa chiyani ukutiyesa opusa ngati ng'ombe? Chifukwa chiyani tikuwoneka ngati opanda nzeru m'maso mwako?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tiyesedwa bwanji ngati nyama za kuthengo, ndi kukhala odetsedwa pamaso panu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa chiyani ukutiyesa ngati ngʼombe ndi kuoneka ngati opusa mʼmaso mwako?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tiyesedwa bwanji ngati nyama za kuthengo, Ndi kukhala odetsedwa pamaso panu?