Job 18:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Nyale ya munthu woipa yazima, malaŵi a moto wake sakuŵalanso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inde, kuunika kwa woipa kudzazima, ndi lawi la moto wake silidzawala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Nyale ya munthu woyipa yazimitsidwa; malawi a moto wake sakuwalanso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inde, kuunika kwa woipa kudzazima, Ndi lawi la moto wace silidzawala.