Job 18:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuŵala kwa m'nyumba mwake kwasanduka mdima, ndipo nyale ya pambali pake yazima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuunikaku kudzada m'hema mwake, ndi nyali yake ya pamwamba pake idzazima.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuwala kwa mʼnyumba mwake kwasanduka mdima; nyale ya pambali pake yazima.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuunikaku kudzada m'hema mwace, Ndi nyali yace ya pamwamba pace idzazima.