Job 19:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu wandikwiyira, akundiyesa ngati mdani wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wandiyatsiranso mkwiyo wake, nandiyesera ngati wina wa adani ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wandikwiyira ndipo akundiyesa mmodzi mwa adani ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wandiyatsiranso mkwiyo wace, Nandiyesera ngati wina wa adani ace.